Numeri 2:15 - Buku Lopatulika15 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 ndipo ankhondo ake ngokwanira 45,650. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650. Onani mutuwo |