Numeri 10:20 - Buku Lopatulika20 Ndi pa gulu la fuko la ana a Gadi anayang'anira Eliyasafu mwana wa Deuwele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndi pa gulu la fuko la ana a Gadi anayang'anira Eliyasafu mwana wa Deuwele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Agadi anali Eliyasafu mwana wa Deuwele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 ndipo Eliyasafu mwana wa Deuweli ndiye ankatsogolera fuko la Gadi. Onani mutuwo |