Numeri 10:19 - Buku Lopatulika19 Ndi pa gulu la fuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiele mwana wa Zurishadai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi pa gulu la fuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiele mwana wa Zurishadai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mtsogoleri wa gulu la Asimeoni anali Selumiele mwana wa Zurishadai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mtsogoleri wa fuko la Simeoni anali Selumieli mwana wa Zurisadai, Onani mutuwo |