Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Numeri 10:23 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la fuko la Manase anali Gamaliele mwana wa Pedazuri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Gamalieli mwana wa Pedazuri ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Manase. |
Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Ndipo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Efuremu, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Elisama mwana wa Amihudi.