Numeri 10:23 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Gamalieli mwana wa Pedazuri ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Manase. Onani mutuwoBuku Lopatulika23 Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Manase anali Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwo |