Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:10 - Buku Lopatulika

10 Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Mwa ana a Yosefe: fuko la Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; fuko la Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri;

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:10
8 Mawu Ofanana  

Wa Benjamini, Abidani mwana wa Gideoni.


Wa Zebuloni, Eliyabu mwana wa Heloni.


Mbendera ya chigono cha Efuremu izikhala kumadzulo monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Efuremu ndiye Elisama mwana wa Amihudi.


Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri.


Tsiku lachisanu ndi chiwiri kalonga wa ana a Efuremu Elisama mwana wa Amihudi:


Tsiku lachisanu ndi chitatu kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa