Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 10:24 - Buku Lopatulika

24 Ndi pa gulu la fuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndi pa gulu la fuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Mtsogoleri wa fuko la Abenjamini anali Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Abidani mwana wa Gideoni ndiye anali mtsogoleri wa mtundu wa Benjamini.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:24
4 Mawu Ofanana  

Wa Benjamini, Abidani mwana wa Gideoni.


Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri.


Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Tsiku lachisanu ndi chinai kalonga wa ana a Benjamini, ndiye Abidani mwana wa Gideoni:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa