Numeri 10:23 - Buku Lopatulika23 Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Manase anali Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Gamalieli mwana wa Pedazuri ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Manase. Onani mutuwo |