Numeri 10:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Efuremu, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Elisama mwana wa Amihudi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Efuremu, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Elisama mwana wa Amihudi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Otsata mbendera ya zithando za fuko la Efuremu adanyamuka m'magulumagulu, ndipo mtsogoleri wa gulu lao anali Elisama mwana wa Amihudi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Magulu a msasa wa Aefereimu anatsatira potsatira mbendera yawo. Elisama mwana wa Amihudi ndiye anali mtsogoleri wawo. Onani mutuwo |