Numeri 1:12 - Buku Lopatulika Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa fuko la Dani, Ahiyezere mwana wa Amishadai; Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ahiyezeri mwana wa Amisadai, kuchokera ku fuko la Dani, |
Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.
Mbendera ya chigono cha Dani izikhala kumpoto monga mwa makamu ao; ndi kalonga wa ana a Dani ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai.