Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:13 - Buku Lopatulika

13 Wa Asere, Pagiyele mwana wa Okarani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Wa Asere, Pagiyele mwana wa Okarani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 fuko la Asere, Pagiyele mwana wa Okarani;

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Pagieli mwana wa Okirani, kuchokera ku fuko la Aseri,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:13
5 Mawu Ofanana  

Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Wa Gadi, Eliyasafu mwana wa Deuwele.


Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani.


Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Asere; ndi kalonga wa ana a Asere ndiye Pagiyele mwana wa Okarani.


Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa