Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:12 - Buku Lopatulika

12 Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 fuko la Dani, Ahiyezere mwana wa Amishadai;

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ahiyezeri mwana wa Amisadai, kuchokera ku fuko la Dani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:12
5 Mawu Ofanana  

Wa Benjamini, Abidani mwana wa Gideoni.


Wa Asere, Pagiyele mwana wa Okarani.


Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Mbendera ya chigono cha Dani izikhala kumpoto monga mwa makamu ao; ndi kalonga wa ana a Dani ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa