Numeri 7:66 - Buku Lopatulika66 Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201466 Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa66 Tsiku lakhumi linali la Ahiyezere mwana wa Amishadai, mtsogoleri wa Adani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero66 Pa tsiku lakhumi Ahiyezeri mwana wa Amisadai, mtsogoleri wa fuko la Dani anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |