Numeri 1:10 - Buku Lopatulika Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwa ana a Yosefe: fuko la Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; fuko la Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri; Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri; |
Mbendera ya chigono cha Efuremu izikhala kumadzulo monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Efuremu ndiye Elisama mwana wa Amihudi.
Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri.