Numeri 2:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Manase, limene mtsogoleri wake ndi Gamaliele mwana wa Pedazuri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Fuko la Manase lidzakhala pafupi ndi Efereimu. Mtsogoleri wa Amanase ndi Gamalieli mwana wa Pedazuri. Onani mutuwo |