Numeri 2:21 - Buku Lopatulika21 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 ndipo ankhondo ake ngokwanira 32,200. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 32,200. Onani mutuwo |