Numeri 2:19 - Buku Lopatulika19 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai kudza mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai kudza mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 ndipo ankhondo ake ngokwanira 40,500. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 40,500. Onani mutuwo |