Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:48 - Buku Lopatulika

48 Tsiku lachisanu ndi chiwiri kalonga wa ana a Efuremu Elisama mwana wa Amihudi:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 Tsiku lachisanu ndi chiwiri kalonga wa ana a Efuremu Elisama mwana wa Amihudi:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Tsiku lachisanu ndi chiŵiri linali la Elisama mwana wa Amihudi, mtsogoleri wa Aefuremu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri Elisama mwana wa Amihudi, mtsogoleri wa fuko la Efereimu, anabweretsa chopereka chake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:48
5 Mawu Ofanana  

Ladani mwana wake, Amihudi mwana wake, Elisama mwana wake,


Wa ana a Yosefe: wa Efuremu, Elisama mwana wa Amihudi; wa Manase, Gamaliele mwana wa Pedazuri.


Mbendera ya chigono cha Efuremu izikhala kumadzulo monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Efuremu ndiye Elisama mwana wa Amihudi.


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Eliyasafu mwana wa Deuwele.


chopereka chake mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa