Ndipo anadziitaniranso khamu la anthu, nanena nao, Mverani Ine nonsenu, ndipo dziwitsani:
Mateyu 23:1 - Buku Lopatulika Pomwepo Yesu analankhula ndi makamu a anthu ndi ophunzira ake, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pomwepo Yesu analankhula ndi makamu a anthu ndi ophunzira ake, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake Yesu adalankhula ndi gulu la anthu ochuluka pamodzi ndi ophunzira ake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Yesu anati kwa magulu a anthu ndi ophunzira ake: |
Ndipo anadziitaniranso khamu la anthu, nanena nao, Mverani Ine nonsenu, ndipo dziwitsani:
Pomwepo pamene anthu a zikwizikwi a khamu anasonkhana pamodzi, kotero kuti anapondana, Iye anayamba kunena kwa ophunzira ake poyamba, Tachenjerani nokha ndi chotupitsa mikate cha Afarisi, chimene chili chinyengo.