Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 22:46 - Buku Lopatulika

46 Ndipo sanalimbike mtima munthu aliyense kumfunsa kanthu kuyambira tsiku lomwelo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Ndipo sanalimbike mtima munthu aliyense kumfunsa kanthu kuyambira tsiku lomwelo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Panalibe ndi mmodzi yemwe wotha kumuyankha ngakhale mau amodzi. Tsono kuyambira tsiku limenelo panalibenso munthu amene adalimba mtima kuti amufunse mafunso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Panalibe wina anatha kuyankha, ndipo kuchokera pamenepo, panalibe wina anayerekeza kumufunsa funso.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:46
12 Mawu Ofanana  

Ndipo anamyankha Yesu, nati, Sitidziwa ife. Iyenso ananena nao, Inenso sindikuuzani ndi ulamuliro wotani ndizichita izi.


Chifukwa chake ngati Davide amtchula Iye Ambuye, ali mwana wake bwanji? Ndipo panalibe mmodzi anatha kumyankha mau.


Ndipo pakuona kuti anayankha ndi nzeru, Yesu anati kwa iye, Suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu. Ndipo palibe munthu analimbanso mtima kumfunsa Iye kanthu.


Ndipo pamene Iye anatero, onse aja akutsutsana naye ananyazitsidwa; ndipo anthu onse a m'khamu anakondwera ndi zinthu zonse za ulemererozo zinachitidwa ndi Iye.


Koma iwo anakhala chete. Ndipo anamtenga namchiritsa, namuuza apite.


Ndipo iwo sanathe kumbwezera mau pa zinthu izi.


Pakuti sanalimbenso mtima kumfunsa Iye kanthu kena.


Ndipotu pakuona munthu wochiritsidwayo alikuimirira pamodzi nao, analibe kanthu kakunena kotsutsa.


akuti, Ine ndine Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abrahamu, ndi wa Isaki, ndi wa Yakobo. Ndipo Mose ananthunthumira, osalimbika mtima kupenyetsako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa