Mateyu 23:2 - Buku Lopatulika2 nanena, Alembi ndi Afarisi akhala pa mpando wa Mose; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nanena, Alembi ndi Afarisi akhala pa mpando wa Mose; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adaŵauza kuti, “Aphunzitsi a Malamulo ndi Afarisi ali ndi udindo wotanthauzira malamulo a Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Aphunzitsi amalamulo ndi Afarisi amakhala pa mpando wa Mose. Onani mutuwo |