Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 23:1 - Buku Lopatulika

1 Pomwepo Yesu analankhula ndi makamu a anthu ndi ophunzira ake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Pomwepo Yesu analankhula ndi makamu a anthu ndi ophunzira ake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pambuyo pake Yesu adalankhula ndi gulu la anthu ochuluka pamodzi ndi ophunzira ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Pamenepo Yesu anati kwa magulu a anthu ndi ophunzira ake:

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 23:1
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anadziitaniranso khamu la anthu, nanena nao, Mverani Ine nonsenu, ndipo dziwitsani:


Pomwepo pamene anthu a zikwizikwi a khamu anasonkhana pamodzi, kotero kuti anapondana, Iye anayamba kunena kwa ophunzira ake poyamba, Tachenjerani nokha ndi chotupitsa mikate cha Afarisi, chimene chili chinyengo.


Ndipo inunso, pa nokha mulekeranji kuweruza kolungama?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa