Mateyu 23:3 - Buku Lopatulika3 chifukwa chake zinthu zilizonse zimene iwo akauza inu, chitani nimusunge; koma musatsanza ntchito zao; pakuti iwo amalankhula, koma samachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 chifukwa chake zinthu zilizonse zimene iwo akauza inu, chitani nimusunge; koma musatsanza ntchito zao; pakuti iwo amalankhula, koma samachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nchifukwa chake muzichita ndi kutsata zonse zimene iwo amakuphunzitsani. Komatu musamatsanzira zimene amachita, pakuti sachita zimene amaphunzitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho muziwamvera ndi kuchita chilichonse chimene akuwuzani. Koma musachite zimene amachita, popeza sachita zimene amaphunzitsa. Onani mutuwo |