Masalimo 81:13 - Buku Lopatulika Ha! Akadandimvera anthu anga, akadayenda m'njira zanga Israele! Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ha! Akadandimvera anthu anga, akadayenda m'njira zanga Israele! Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Anthu anga akadandimvera, Aisraele akadayenda m'njira zanga, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Anthu anga akanangondimvera, Israeli akanatsatira njira zanga, |
Mwenzi utamvera malamulo anga mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje, ndi chilungamo chako monga mafunde a nyanja;
Koma sanamvere, sanatchere khutu, koma anayenda mu upo ndi m'kuuma kwa mtima wao woipa, nabwerera chambuyo osayenda m'tsogolo.
Ha, Yerusalemu, Yerusalemu, amene umapha aneneri, ndi kuwaponya miyala iwo otumidwa kwa iwe! Ine ndinafuna kangati kusonkhanitsa pamodzi ana ako, inde monga thadzi lisonkhanitsa anapiye ake m'mapiko ake, koma inu simunafune ai!
Ha? Mwenzi akadakhala nao mtima wotere wakundiopa Ine, ndi kusunga malamulo anga masiku onse, kuti chiwakomere iwo ndi ana ao nthawi zonse!