mbalame za m'mlengalenga, ndi nsomba za m'nyanja. Zopita m'njira za m'nyanja.
mbalame zamumlengalenga, nsomba zam'nyanja, ndi zonse zoyenda pansi pa nyanja.
mbalame zamlengalenga ndi nsomba zamʼnyanja zonse zimene zimayenda pansi pa nyanja.
Kodi ukhoza kusakira mkango waukazi nyama? Ndi kukwaniritsa chakudya cha misona,
Tapenya tsono mvuu ndinaipanga pamodzi ndi iwe, ikudya udzu ngati ng'ombe.
Nyama zakuthengo ndi zoweta zonse; zokwawa, ndi mbalame zakuuluka.