Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 8:7 - Buku Lopatulika

7 nkhosa ndi ng'ombe, zonsezo, ndi nyama zakuthengo zomwe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 nkhosa ndi ng'ombe, zonsezo, ndi nyama za kuthengo zomwe;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 nkhosa, ng'ombe ndi nyama zakuthengo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 nkhosa, mbuzi ndi ngʼombe pamodzi ndi nyama zakuthengo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 8:7
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m'chifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe chathu: alamulire pansomba za m'nyanja, ndi pambalame za m'mlengalenga, ndi pang'ombe, ndi padziko lonse lapansi, ndi pazokwawa zonse zakukwawa padziko lapansi.


Mulungu ndipo anadalitsa iwo, ndipo adati kwa iwo, Mubalane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi, muligonjetse: mulamulire pansomba za m'nyanja, ndi pambalame za m'mlengalenga, ndi pazamoyo zonse zokwawa padziko lapansi.


Adamu ndipo anazitcha maina zinyama zonse, ndi mbalame za m'mlengalenga ndi zamoyo zonse za m'thengo: koma kwa Adamu sanapezeke womthangatira iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa