Masalimo 8:8 - Buku Lopatulika8 mbalame za m'mlengalenga, ndi nsomba za m'nyanja. Zopita m'njira za m'nyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 mbalame za m'mlengalenga, ndi nsomba za m'nyanja. Zopita m'njira za m'nyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 mbalame zamumlengalenga, nsomba zam'nyanja, ndi zonse zoyenda pansi pa nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 mbalame zamlengalenga ndi nsomba zamʼnyanja zonse zimene zimayenda pansi pa nyanja. Onani mutuwo |