Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 8:9 - Buku Lopatulika

9 Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga pa dziko lonse lapansi!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Chauta, Ambuye athu, dzina lanu ndi lotchuka pa dziko lonse lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Inu Yehova, Ambuye athu, dzina lanu ndi lamphamvudi pa dziko lonse lapansi!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 8:9
4 Mawu Ofanana  

Kodi ukhoza kupeza Mulungu mwa mufunafuna? Ukhoza kupeza Wamphamvuyonse motsindika?


Ntchito zanu zichulukadi, Yehova! Munazichita zonse mwanzeru; dziko lapansi lidzala nacho chuma chanu.


Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi! Inu amene munaika ulemerero wanu pa thambo la kumwamba.


Palibe wina ngati Mulungu, Yesuruni iwe, wakuyenda wokwera pathambo, kukuthandiza, ndi pa mitambo mu ukulu wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa