Masalimo 9:1 - Buku Lopatulika1 Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; ndidzawerengera zodabwitsa zanu zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; ndidzawerengera zodabwitsa zanu zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndidzakuthokozani, Inu Chauta, ndi mtima wanga wonse. Ndidzasimba za ntchito zanu zonse zodabwitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ine ndidzakutamandani, Inu Yehova, ndi mtima wanga wonse; ndidzafotokoza za zodabwitsa zanu zonse. Onani mutuwo |