Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni.
Mitundu yonse ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu, mitundu yonse ya anthu ikuyamikeni.
Mitundu ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu; mitundu yonse ya anthu ikutamandeni.
Ndipo Yehova adzakhala msanje kwa iye wokhalira mphanthi. Msanje m'nyengo za nsautso;
Ndipo kudzatero, ukamuka nafe, inde, kudzali kuti zokoma zilizonse Yehova atichitira ife, zomwezo tidzakuchitira iwe.