Numeri 10:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo kudzatero, ukamuka nafe, inde, kudzali kuti zokoma zilizonse Yehova atichitira ife, zomwezo tidzakuchitira iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo kudzatero, ukamuka nafe, inde, kudzali kuti zokoma zilizonse Yehova atichitira ife, zomwezo tidzakuchitira iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Mukapita nao, zilizonse zimene Chauta adzatichitire, ife tidzakuchitirani zomwezo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Iweyo ukapita nafe, tidzagawana nawe zinthu zabwino zomwe Yehova adzatipatsa.” Onani mutuwo |