Numeri 10:31 - Buku Lopatulika31 Koma anati, Usatisiyetu; popeza udziwa poyenera kumanga ife m'chipululu, ndipo udzakhala maso athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma anati, Usatisiyetu; popeza udziwa poyenera kumanga ife m'chipululu, ndipo udzakhala maso athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo Mose adati, “Musatisiye, ndapota nanu, poti inu mukudziŵa kumene tingamange mahema m'chipululu muno, ndipo mudzakhala maso athu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndipo Mose anati, “Pepa usatisiye popeza ukudziwa kumene tingamange misasa mʼchipululu muno ndipo udzakhala maso athu. Onani mutuwo |