Masalimo 148:2 - Buku Lopatulika Mlemekezeni, angelo ake onse; mlemekezeni, makamu ake onse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mlemekezeni, angelo ake onse; mlemekezeni, makamu ake onse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtamandeni inu angelo ake onse, mtamandeni inu magulu a ankhondo ake onse! Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mutamandeni, inu angelo ake onse, mutamandeni, mutamandeni, inu zolengedwa za mmwamba. |
muja nyenyezi za m'mawa zinaimba limodzi mokondwera, ndi ana onse a Mulungu anafuula ndi chimwemwe?
Pamenepo mzimu unandinyamula, ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mau a mkokomo waukulu, ndi kuti, Wodala ulemerero wa Yehova m'malo mwake.