Chilichonse dzanja lako lichipeza kuchichita, uchichite ndi mphamvu yako; pakuti mulibe ntchito ngakhale kulingirira ngakhale kudziwa, ngakhale nzeru, kumanda ulikupitako.
Masalimo 132:3 - Buku Lopatulika Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, ngati ndidzakwera pa kama logonapo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, ngati ndidzakwera pa kama logonapo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Ndithu sindidzaloŵa m'nyumba mwanga, kapena kukagona pabedi panga, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Sindidzalowa mʼnyumba mwanga kapena kugona pa bedi langa: |
Chilichonse dzanja lako lichipeza kuchichita, uchichite ndi mphamvu yako; pakuti mulibe ntchito ngakhale kulingirira ngakhale kudziwa, ngakhale nzeru, kumanda ulikupitako.
Kodi imeneyi ndiyo nthawi yakuti inu nokha mukhala m'nyumba zanu zochingidwa m'katimo, ndi nyumba iyi ikhale yopasuka?
Koma muyambe mwafuna Ufumu wake ndi chilungamo chake, ndipo zonse zimenezo zidzaonjezedwa kwa inu.