Masalimo 132:4 - Buku Lopatulika4 ngati ndidzalola maso anga agone, kapena zikope zanga ziodzere; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ngati ndidzalola maso anga agone, kapena zikope zanga ziodzere; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 sindidzalola kuti ndikhale m'tulo kapena kuti zikope zanga ziwodzere, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 sindidzalola kuti maso anga agone, kapena zikope zanga ziwodzere, Onani mutuwo |