Masalimo 132:3 - Buku Lopatulika3 Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, ngati ndidzakwera pa kama logonapo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, ngati ndidzakwera pa kama logonapo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 “Ndithu sindidzaloŵa m'nyumba mwanga, kapena kukagona pabedi panga, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Sindidzalowa mʼnyumba mwanga kapena kugona pa bedi langa: Onani mutuwo |