Ndipo Davide anakhala m'linga muja, nalitcha mzinda wa Davide. Davide namanga linga pozinga ponse kuyambira ku Milo ndi m'kati momwe.
Masalimo 122:3 - Buku Lopatulika Yerusalemu anamangidwa ngati mzinda woundana bwino: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yerusalemu anamangidwa ngati mudzi woundana bwino: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yerusalemu adamangidwa bwino, zigawo zake zonse nzogwirizana pamodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yerusalemu anamangidwa ngati mzinda umene uli wothithikana pamodzi. |
Ndipo Davide anakhala m'linga muja, nalitcha mzinda wa Davide. Davide namanga linga pozinga ponse kuyambira ku Milo ndi m'kati momwe.
Koma tinamanga lingali, ndi linga lonse linalumikizana kufikira pakatimpakati; popeza mitima ya anthu inalunjika kuntchito.