Masalimo 122:2 - Buku Lopatulika2 Mapazi athu alinkuima m'zipata zanu, Yerusalemu Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mapazi athu alinkuima m'zipata zanu, Yerusalemu Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mapazi athu akhala akuima m'kati mwa zipata zako, iwe Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mapazi athu akuyima mʼzipata zako, Iwe Yerusalemu. Onani mutuwo |