Masalimo 122:3 - Buku Lopatulika3 Yerusalemu anamangidwa ngati mzinda woundana bwino: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Yerusalemu anamangidwa ngati mudzi woundana bwino: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yerusalemu adamangidwa bwino, zigawo zake zonse nzogwirizana pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yerusalemu anamangidwa ngati mzinda umene uli wothithikana pamodzi. Onani mutuwo |