Masalimo 118:3 - Buku Lopatulika Anene tsono nyumba ya Aroni, kuti chifundo chake nchosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Anene tsono nyumba ya Aroni, kuti chifundo chake nchosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Banja la Aroni linene kuti, “Chikondi chake nchamuyaya.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Banja la Aaroni linene kuti, “Chikondi chake ndi chosatha.” |
inunso ngati miyala yamoyo mumangidwa nyumba ya uzimu, kuti mukhale ansembe oyera mtima, akupereka nsembe zauzimu, zolandiridwa ndi Mulungu mwa Yesu Khristu.
natiyesa ife ufumu tikhale ansembe a Mulungu ndiye Atate wake; kwa Iye kukhale ulemerero ndi mphamvu kufikira nthawi za nthawi. Amen.