Masalimo 118:2 - Buku Lopatulika2 Anene tsono Israele, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Anene tsono Israele, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Aisraele anene kuti, “Chikondi chake nchamuyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Israeli anene kuti: “Chikondi chake ndi chosatha.” Onani mutuwo |