Masalimo 118:1 - Buku Lopatulika1 Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Thokozani Chauta chifukwa ngwabwino, ndipo chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yamikani Yehova chifukwa ndi wabwino; pakuti chikondi chake chosasinthika ndi chosatha. Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.