Masalimo 118:3 - Buku Lopatulika3 Anene tsono nyumba ya Aroni, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Anene tsono nyumba ya Aroni, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Banja la Aroni linene kuti, “Chikondi chake nchamuyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Banja la Aaroni linene kuti, “Chikondi chake ndi chosatha.” Onani mutuwo |