Masalimo 118:4 - Buku Lopatulika4 Anene tsono iwo akuopa Yehova, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Anene tsono iwo akuopa Yehova, kuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Anthu oopa Chauta anene kuti, “Chikondi chake nchamuyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo amene amaopa Yehova anene kuti: “Chikondi chake ndi chosatha.” Onani mutuwo |