Masalimo 118:5 - Buku Lopatulika5 M'mene ndinasautsika ndinaitanira pa Yehova; anandiyankha nandiika motakasuka Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 M'mene ndinasautsika ndinaitanira pa Yehova; anandiyankha nandiika motakasuka Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamene ndinali m'mavuto ndidapemphera kwa Chauta, ndipo Iye adandichotsera mavutowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndili mʼmasautso anga ndinalirira Yehova, ndipo Iye anayankha pondichotsa mʼmasautsowo. Onani mutuwo |