Pakuona Yowabu tsono kuti nkhondo inamdzera kumaso ndi kumbuyo, anasankha amuna osankhika onse a Israele, nawanika ayambane ndi Aaramu.
Masalimo 118:11 - Buku Lopatulika Adandizinga, inde, adandizinga: Indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Adandizinga, inde, adandizinga: Indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adandizinga, inde adandizinga pa mbali zonse, koma ndidaŵaononga ndi mphamvu za dzina la Chauta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anandizinga mbali zonse, koma mʼdzina la Yehova ndinawawononga. |
Pakuona Yowabu tsono kuti nkhondo inamdzera kumaso ndi kumbuyo, anasankha amuna osankhika onse a Israele, nawanika ayambane ndi Aaramu.
Ndipo Saulo anamuka mbali ina ya phiri, Davide ndi anthu ake kuseri kwake; ndipo Davide anafulumira kuthawa, chifukwa cha kuopa Saulo; popeza Saulo ndi anthu ake anazinga Davide ndi anthu ake kwete kuti awagwire.