Ndipo Efuroni anakhala pakati pa ana a Hiti, ndipo Efuroni Muhiti anayankha Abrahamu alinkumva ana a Hiti, onse amene analowa pa chipata cha mzinda wake, kuti,
Luka 2:3 - Buku Lopatulika Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumzinda wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumudzi wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero anthu onse adapita kukalembedwa, aliyense ku mudzi kwao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo aliyense anapita ku mzinda wa kwawo kukalembetsa. |
Ndipo Efuroni anakhala pakati pa ana a Hiti, ndipo Efuroni Muhiti anayankha Abrahamu alinkumva ana a Hiti, onse amene analowa pa chipata cha mzinda wake, kuti,
Ndipo kunali masiku aja, kuti lamulo linatuluka kwa Kaisara Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe;
Ndipo Yosefe yemwe anakwera kuchokera ku Galileya, kumzinda wa Nazarete, kunka ku Yudeya, kumzinda wa Davide, dzina lake Betelehemu, chifukwa iye anali wa banja ndi fuko lake la Davide;
kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Maria, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu anali ndi pakati.