Luka 2:2 - Buku Lopatulika2 ndiko kulembera koyamba pokhala Kwirinio kazembe wa Siriya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndiko kulembera koyamba pokhala Kwirinio kazembe wa Siriya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kalembera ameneyu anali woyamba, ndipo adachitika pamene Kwirinio anali bwanamkubwa wa dziko la Siriya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 (Uyu ndi kalembera woyamba amene anachitika pamene Kureniyo anali bwanamkubwa wa Siriya). Onani mutuwo |