Luka 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumzinda wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumudzi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Motero anthu onse adapita kukalembedwa, aliyense ku mudzi kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo aliyense anapita ku mzinda wa kwawo kukalembetsa. Onani mutuwo |