Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 2:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ndipo aliyense anapita ku mzinda wa kwawo kukalembetsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumzinda wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo onse anamuka kulembedwa, munthu aliyense kumudzi wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Motero anthu onse adapita kukalembedwa, aliyense ku mudzi kwao.

Onani mutuwo Koperani




Luka 2:3
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo nʼkuti Efroni Mhiti ali pomwepo pakati pa anthuwo amene anabwera ku chipata cha mzindawo. Ndipo onse akumva anamuyankha Abrahamu


Mʼmasiku amenewo Kaisara Augusto anapereka lamulo kuti kalembera achitike mʼdziko lonse la Aroma.


(Uyu ndi kalembera woyamba amene anachitika pamene Kureniyo anali bwanamkubwa wa Siriya).


Choncho Yosefe anachoka ku Nazareti ku Galileya kupita ku Yudeya, ku Betelehemu ku mudzi wa Davide, chifukwa anali wa banja ndi fuko la Davide.


Iye anapita kumeneko kukalembetsa pamodzi ndi Mariya, amene anapalana naye ubwenzi kuti akwatirane ndipo anali woyembekezera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa